Kasonkhanitsidwe ka mitundu ya Adyo

Zokhudza ntchotoyi

Cholinga cha tsambali ndikubweretsa uthenga okwanira pa mitundu ya Adyo ya dziko lonse lapansi, komaso kukonza misika ya Adyo wa pamwamba Yabwino wambeu komaso wakudya.

Tigaileni mitundu ya Adyo wa kwanuko!

Kodi mumadzala mtundu wa Adyo wongoyenera kudera kwanu kokhako kapena wamakolo? Titumizileni zithunzi komanso uthenga okhudzana ndi Adyo ameneyi. Ife tidzaziika izi mu Kasonkhanitsidwe ka mitundu ya Adyo ndi msangala.

Tidzakondwera ngati mungatumize Adyo wambiri wapayekhapayekha kapena wa m’maphava ku Nkhokwe ya nthanga ndi zomera. Tizamuchulukitsa kenaka ndikugawana ndi athu ena amene ali ndi chidwi pa Adyo.

Registration in the mailinglist

Your email:
Your country
Your language

Copyright © 2015–2018 Kasonkhanitsidwe ka mitundu ya Adyo M’ndandanda wa mitundu ya Adyo
Follow us on Facebook
Last update: 03. Okutobala 2018